Dan Lu - Daily (Prod. Rockers Records)
Name of album : Daily Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro
Yaka yaka yoo
Life life yandipatsa nyimbo
Life

Verse 1
Akanakhala amaonda ndikunenedwa
Bwenzi ntatsala fupa ndikuvala thewera
Anthu ali ndi nsambi Kunja kuno
Pena ukamva nkhani yako, kulephera kudya kumene
Ataikazingira, kuithira anyeziii
Kuifaka kamchereee, ikumvekera bwino
Iwe kulephera kulongosola, Kuzibakila
Ulipo wekhaa, chigulu chachiluka

Chorus
Mbuye mbuye mukhale nane
Daily daily daily aaah
Dziko lindimeza ilii mmh
Kamoyoka kasungeni
Daily daily daily aah
Akuopsa ndimunthu lero
Kuposa nkhwere
Mbuye muyende nane
Daily daily daily aahh
Daily daily daily daily daily daily ambuye
Kamoyoka kasungeni
Daily daily daily aahh
Anawa inee ooh oooh

Verse 2
Ndimatha kuona chipiringu mtatseka maaaso
Ambiri ofuna kuona zoona mchawa wapitadi
Ndimatha kuona momwe nkhuku zikukhwasuliiidwa
Kunyadira kupita kwanga coz they were under pressure

Pamaso kukusekelera
Kumbali ndiwe laughing stock
Pamaso kukusekelera
kumbali ndiwe laughing stock

Apa mpomwe umadziwa blood thicker than water
Thank you my darling, Thank you my family
There’s no turning back we here to stayyy
Tricky, am feeling am feeling am feeling this beat yeah

Chorus
Mbuye muyende nanee
Daily daily dily daily
Dziko lindimeza ili ili ili
Kamoyoka kasungeni
Daily daily daily aaah
Akuopsa ndimunthu lero, kuposa njoooka
Mbuye mukhale nanee
Daily daily daily daily
Oh Nono Oh Nono Oh Nono Oh Nono Oh Nono
Kamoyo kasungeni
Daily daily daily aaaah
Kasungeni daily daily daily
Kasungeni daily daily daily