Dapa - Bola Hule
Name of album : Issuez II Genre :RnB
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Chorus
Bola hule (Bola Hule echo)
Kakumpanda ufapo wabule
Better da devil u knw dan da angel u dnt
Bola hule (Bola hule echo)
Kakumpanda ufapo ulele
Better da devil u knw dan angel u dnt

Verse 1
Ati ndagwila kanyatwa 
Kakumpanda inu kofatsa
Kampaketi nditsegula ngekha
Palibeso wina amalasa
Chosadziwa (dziwa)magalimoto amachita kusinthana (kusinthana)
Azibambo kuchita kulimbilana
Ngati chaulele inu chimanga inu chimanga

Bridge
Takumpanda ndiitima pretenders
Tatopa ndikuchotsa zimimbazi
Udyapo chabe ma remainders 
Aazimbambo akupatsila zinthendazi

Chorus

Verse 2
Banja la mtsogolo lake liti lomwe saakadziwa
Mimba!!! yoyamba ku Lilongwe
Mimba!!! yachiwiri ku phalombe
Mimba!!! yachitatu ku nsanje
Mimba!!! yachinayi ku bangwe
Ndikungochenjezapo chabe ine si nsanje si nsanje si nsanje
Blidge
chorus