Taurai - Sindinadziwe (Prod by Don Foxxy & Don T)
Name of album : Sindinadziwe Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


*Intro*

Sin'nadziwe...(x2

*_Taurai..._*

*Verse 1*

Ankatonena'wo
Malaya ndi amodzi iwe
Ankatokamba'wo
Kabudula zigamba tho!
Ati sitepe yako
Pobwera ngati ukupita Ankakutcha _pewani_ iwe
Ankati 'Love is Blind'
Pa iweyo ndinabetsa eeh
Ankayesa nditekeseka ine
Ona lero mitu angopukusa aah
Sakumvetsa...
Lero ankhoswe nkhuku akhadzulirana

*Chorus*

Sindinadziwe eyaye kuti kukhala kuli choncho.
(Sindinadziwe eyaye kuti kukhala kuli choncho).
Kundinyozera mamuna inuyo
Ine zimenezo nde toto...
Ndakonda yemweyu ineyo
Yemwe azandisunge.

*Verse 2*

Akanadziwa sakananeena
You're my everything
My honey'wo
My sugar sugar (x2)

M'maluzi tikhala imodzi
(Limodzi...)
M'mawini tikhala limodzi
(Limodzi...)
Coz you're my everything
My honey'wo
My sugar sugar yeeee-yeeeh

*Chorus*

Sindinadziwe eyaye
Kuti kukhala kuli choncho
(Sindinadziwe eyaye
Kuti kukhala kuli choncho)
Kundinyozera mamuna inuyo
Ine zimenezo nde toto (Ndakonda emweyu ineyo
Yemwe azandisunge)

*Bridge*

Ankatonena'wo
Malaya ndi amodzi iwe Akanadziwa Sakananeena
Akanadziwa Sakananeena
You're my everything
My honey'wo
My sugar sugar
M'mawini tikhala limodzi
(Aaayeeee)
M'maluzi tikhala limodzi
(Aayeee)
Coz you're my everything
My honey'wo
My sugar sugar heeh!!!! Iyeee
Ooooh

*Chorus*

Sindinadziwe eyaye
Kuti kukhala kuli choncho
(Sindinadziwe eyaye
Kuti kukhala kuli choncho)
Kundinyozera mamuna inuyo
Ine zimenezo nde toto
(Ndakonda yemweyu ineyo
Yemwe adzandisunge) (x2)

Ng'yakuthanda wena
Ng'yakuthanda mina
Eee umuntu wami.