24014Downloads
PQ - Sindidzakula [Feat Krazie G & Martse] (Prod. Janta)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Sindidzakula ine sindidzasintha ine
Nthawi zonse kuphaka life
Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine
Nthawi zonse kusaka wife
Verse 1 Krazie G
Ndina blower!! Easy kaye guys
Ndiwonetseni yanga nditi size
Ndikapha iyi mundipasa prize
Ndimafika pa 21 ndika roller dice Aaah izi
Ndinazolowera kupanga
Usanditchalenje ndinkazi wako mphwanga
Mapeto wake ndimupatsa phaaa
Akabwera paden ine ndizamukana
Am just chilling by my crib
Like it’s just ok and you know what
I just made it to day and I told her
am CRAZY lil’ something like Jay Z
Hook
Sindidzakula ine sindidzasintha ine
Nthawi zonse kuphaka life
Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine
Nthawi zonse kusaka wife
Verse 2 (PQ)
Sindidzakula aise Sindidzakula aise
Zimene ndikugwetsa pano kuposa mvula ise
Olo kulankhula kokha ngati m’busa
Olo nkazi wakoyo nditha kugwetsa aise
Ukuseka aise Ukuseka aise
Ukuyesa ngati ndikucheza aise
Tangoyesa aise tangoyesa aise
Uzalira pa mawa cha mma 10 aise
Wait izi ndizabawa
Sindikufuna mpaka zivute pa mawa
Koma ndilibe nkhawa
Ofcoz ndayaka
Hook
Sindidzakula ine sindidzasintha ine
Nthawi zonse kuphaka life
Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine
Nthawi zonse kusaka wife
Verse 3 (Martse)
Sindine mamas bwoy
Ndine mama star bwoy
Ngati ukutsutsa izo nde ndizako
Sindidzakula ndili pa Sunday school
Ndine mfana wausilu ndili ndi akazi 2
Mukuzimva kukula bwanji mupepere
Ngati Varles Kamzere bwanji munyeredwe
Umatha ku baker cake nkazi ibekedwe
Akunyoza ineyo bwanji asekedwe
Anthu akundisaka eya ndili pa market
Akazi amandikonda nkhale ndimamwa masachet
Martse ofanana ndi masten
Nkhani yanyimbo anatenga 10 pa 10 Freshmen!!
Hook
Sindidzakula ine sindidzasintha ine
Nthawi zonse kuphaka life
Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine
Nthawi zonse kusaka wife