Piksy - Mwezi Uwale
Name of album : Mthunzi Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


HOOK
Mwezi uwale eh
Ndikumane ndi dona apa
Lija ndi kale eh
Mfundo zanga ndiponya apa
BRIDGE
Kapena ndimenye bibida?
Mantha ndiye andidinda
Ndikumva ngati ndadzimbidwa
Pompano nditha kubibidwq
VERSE 1
Sikapatali kadonaka nkapatsidyapa
She's never heard of me zokuti ndimachita cha
She's on point
Nkowala ngati dzuwa
Nde kamachita kudziwa
Koma ulemu wokhawo
She is more like an angel
She z beautiful and humble
Duwa duwa bambo
Kukongola kwake kunabwera mma bundle
Hmm
Mano okhawo ndi malonda a colgate
Uyu yekha ndichita zotheka akhale soul mate
HOOK
Mwezi uwale
Ndikumane ndi douner apa
Lija ndi kale
Mfundo zanga ndiponya apa
VERSE 2
Anzanga andiuza zimafunika kufewa
Koma ena andiuza nzongofunika kupewa
Malangizo onsewa
Ndinene mosanama andipangisa kufeela ngati mbewa
At some point its true
Kukanidwa nkowawa nkamuuziratu zikhale zodziwa anthu two
Apo biii....
No i wouldn't hurt her
She wdnt hate me
I wouldn't let her
Chomwe ndufuna ndi chikondi
Nothin more
Sindziwa za mawa but i know i will be the best man she won't need another
Her man and her brother
Awesome couple ya pa magazine cover
We gonna travel the world
i mean every word
Anthu adzatitchula love birds
Chikondi cha muyaya it will never end
NaBola akongolola
HOOK
Mwezi uwale
Ndikumane ndi douner apa
Lija ndi kale
Mfundo zanga ndiponya apa
Chikondi changa nchokoma ulawe
Ndimafunitsitsa ntadziwana nawee
Ndikakuwona ngati ndithaawe
Kukanika kulimba mtima
Mutuwu umaima
BRIDGE
Kapena ndimenye bibida?
Mantha ndiye andidinda
Ndikumva ngati ndadzimbidwa
Pompano nditha kubibidwq
HOOK
Mwezi uwale
Ndikumane ndi douner apa
Lija ndi kale
Mfundo zanga ndiponya apa