Clemo Tryphks - Ndilibe Chikondi
Name of album : Singles Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO
Uu yeah pepani chemwali
Pepani adona
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowa
Ndilibe ndilibe ehy!

#HOOK
Pepani chemwali×2
Pepani adona×2
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowa
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowaaa ah

#VS 1
Chikondi kuchi-player
Chikondi kuchiyesa
Usalire poti wabetsa
Usalire pot waliza
Chikondi nchotani
Mtima ndiotani
Ndinali ofatsa odekha
,odekha,izi ndi izi ine ayi
Koma leronso mwaliwe
Wandifunaso bwanjiwe
Ndilibe chikondiwe
Ndilibenso mpata owe
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowa
chikondi ndilibe
Chikondi ndisowaa

#HOOK HOOK HOOK
#HOOK HOOK
#HOOK

Chemwali pepani ndithu
Chikondi sima-share
U need to take care
Komaso kunvetsetsa
Nakuuza izi leka
Nasamala iwe wekha
Nakuuza udzalira
Iweyo udzandisowa
Chikondi ndinali nacho
Pa iwe anga maso
Pepani ndilibe kaso
Poti mtima waswekaso
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowa
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowaa

#HOOK HOOK HOOK
#HOOK HOOK
#HOOK

#BRIDGE
Uu yeah pepani chemwali
Pepani adona
Chikondi ndilibe
Chikondi ndisowa
Ndilibe ndilibe ehy!

#HOOK HOOK HOOK
#HOOK HOOK
#HOOK
BAKINGZ;;;inu
Inu
Sortie
Babie
Sortie
Babie