21240Downloads
Azizi - Ma Tippex (Prod. Fiuke Jam Records)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
A2121 ee aaa aah ah
Chorus
Ichi chikondi ndichomasukirana ndichopanda madando sichopaka ma Tippex
Or akwao sangabwere kwathu mkudzachita mavando chilibepo ma tippex
Owo owo owo sichopaka ma tippex
Owo owo owo chilibe ma tippex
Ichi chikondi ndichomasukurana ndichopanda madando sichopaka ma tippex
Or akwathu sangapite kwa mkukapanga mavando sichopaka ma tippex
Owo owo owo sichopaka ma tippex
Owo owo owo chilibe ma tippex,
Verse 1
Chisankho chako mchanga chisankho changa mchako oo no mistake,
Ndizifukwa zokwana ukuliyambe banjaaa tikadye biscuit,,
Awo ankandikana pano akundikonda chonchi bwanji aika Tippex,,
Asusukira otchuka chikondi chawo asinthitsa ndi ndalama ali cheapest,,
Bridge
Chikondi chaiwe ndiineyo ayi mchosapaka Tippex,,
Ndipo iwe usankha ineyo ayi sudachite mistake,,
Back to CHORUS,
Verse 2
Chikondi sachonderera aliyese azimasuka sendera sendera,
Asakupatse madandaulo mtima wako munchikondi ukhale okondwera,
Narrow & void chikondi cha tippex,
Chingauike moyo wako pa risky,
Kukonda osakukonda dats a mistake,,
Umukonde oti akuuze,,,
Bridge