3024Downloads
Soul Raiders Band - Chikhalidwe
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Mtima wanga sukumvesa/ msonzi yokha ikungogwa
Maso anga atopa sakuona
Chisoni change ndi fuko langa/ dzukani osagona
Mtundu kutha inu mukuona
Oposa sazindikira/ anzeru adanka kuti
Miyambo yachikuda/ kutengera zitisambula
Pakuti ife/ oah oah eih eyah
Chorus
Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera
Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera
Chete wanga sikupusa/ musandiwete ngati galu
I got the right to say whats on my mind
Ndinu nomwe mwachita izi/ ngakhale mwana akudziwa
Nanga inu osangovomera
Mukulemekeza alendo/ kuwapasa chuma ndi malo
Eni nthaka/ kwao ndi kupemphapempha basi
Katangale ndi ziphuphu/ kusakhulupirika udindo
Eni nthaka/ kupwetekana tokhatokha basi
Chorus
Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera
Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera