Click here to download this song >> Desktop | Mobile
INTRO
Yakayakayo Mayar noel / dan lu / malawian boy pon g on tha board ( Inenso ndi shasha entertainment !!!!! )yakayakayo
Chorus 1
Usandiletse kunjoya beib / moyo ndi waufupi iwu moyo ndi waufupi /
ine ndinjoya hun mamamama/ ine ndinjoya mam mamamama /
ndinjoya beib mamamama
Verse 1
Let’s do it tonight let’s pop bottles / yea am in the club doin my bottles /
Where my girls at the party boy is about to go live to night /
Go go go go go down low / shake that booty go downlow /
Grab a beer take a beer meet me othe sofa/ lets drink this /am a big fish
zabwino ziri mkati kunjaku tikuchedwa / gwedeza mu ka min madzulo ukuphedwa /
mbina yake imenei koma tilimba/ mwendo wake umuneu koma tiyimba/
akazi akubwera ndikumenya bacrays/ ndingogwira ndi kudoda ndine keaper bathez /
Matter of fact I don’t live in fear / undikambe undikambe I belive in beer.
Chorus 2
Usandiletse kunjoya beib / moyo ndi waufupi iwu moyo ndi waufupi /
ine ndinjoya hun mamamama/ ine ndinjoya mam mamamama /
ndinjoya beib mamamama / sindikutopa ndabwera onkonzeka mamamama /
kuvina mpaka thukuta mamamama / beib pano pavuta mamamamam/
eeee ee kuku kuzipepesa mamamama / money kumangomwaza mamamama/
thukuta kumangokhesa mamamam/ beib yelele
verse 2
ndili pompoka / kusinjira chidakwa chiomboka
apapa zilimu ndi ee mboba / ndikasochera mundiimbire hangover /
what? kulankula ndi mizimu / mkunda wachiwiri zililimu /
shot ya chi 11 ndikwanilitsa team / eti kusemphana ngati card ndi sim/
apa mwali ndingopepesa / zokugwira mbinazo ungomvesetsa /
kodi mkatimu chilesi wajampisa/ lero ndikagona kwanu mwendo tenthesa /
uhule suli mmowa ukakonzeka chiuno tikuthowa/ tingomwalira tonse my leg is up chin’goma chikatele ku dowa.
Chorus 3
Usandiletse kunjoya beib / moyo ndi waufupi iwu moyo ndi waufupi u/
ine ndinjoya hun mamamama/ ine ndinjoya mam mamamama /
ndinjoya beib mamamama / sindikutopa ndabwera onkonzeka mamamama /
kuvina mpaka thukuta mamamama / beib pano pavuta mamamamam/
eeee ee kuku kuzipepesa mamamama / money kumangomwaza mamamama/
thukuta kumangokhesa mamamam/ beib yelele
Bridge
I feel like my body is on fire x2
I feel like my body – aa , I feel like- okyy
I feel like my body is on fire x 3
Chorus 3
Usandiletse kunjoya beib / eeeeeee
mamamama/ mam mamamama /
ndinjoya beib mamamama / sindikutopa ndabwera onkonzeka mamamama /
kuvina mpaka thukuta mamamama / beib pano pavuta mamamamam/
eeee ee kuku kuzipepesa mamamama / money kumangomwaza mamamama/
thukuta kumangokhesa mamamam/ beib yelele
outro
noel/ dan malawian boy
lalalalala mmmm yakayakayo
ayeyeyeyey ayeyeye ayeyeyey eeee
inenso ndi shasha entertainment