Charisma - Mabodza
Name of album : Mabodza Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


(Intro)
Yayayayayah
Ya ya
Yayayayayah
Ya ya

Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah
Ankati ineyo ndi mfana Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah

(Verse 1)
Ndinablowa ndikubanda
Koma ndimadana ndiza chamba
Sine mfana wamumpanda
But I got skills in abundance
Mwina ndi zomwe ndimamangazi
Kapena pasha ndimavalayi
Kwa ine akazi ndima dalazi
Kwa ine akazi ndima dalazi
Yea kumenya ma hit back to back track on track
Rapper kubwela kupanga attack attack
Koma osamuyakha ine si size yake
Pitani mukauzane simungamake

(Hook)
Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah
Ankati ineyo ndi mfana Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah

(Verse 2)

See the DJ play my song at the bar
I'm a star, understand
I'm baba voss gimme props no jokes
Don't you ever cross me inkosi yamakosi
Call me Kris Kross, offwhite socks
White airforce, sports car two doors
I pay my bills no bankrupt
Mr money ndili instant
Ask your girls ndine merchant
Mu new school ndine legend
Since 2016 I've been rapping for my team
20-20 vision now I'm living my dream wusup

(Hook)
Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah
Ankati ineyo ndi mfana Mabodza
chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama
Yayayayayah

(Outro)
Hahaha ayeh madness
Yayayayayah
Ya ya
Yayayayayah
Ya ya