82Downloads
Kim Deezy - Punch After Punch

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Ya' already know what it is
It's Kim Deezy Eazy
Slapping these whack rappers
With Punch after Punch one more time!
Kudzuka mmawa kuyang'ana kwagwanji
Palibe chagwa ndiye ndigwetsa punch
Ndidzipange introduce kapena mumandiyada?
Kupanga zaineyo ndeti mbiliyako yada
Ndidzakusukuludza
Ma hater alipo ambiri akudabwa siukuluza
Pa beat ndima spinner TOYOTA cruiser
OG salowelela zosamukhuza
Musakanene bodza apatilitonse
Ine sindiopa tima rapper tilitonse
Amadzimva u Young king nde dikila tiatonse
Kutchuka ndikwanu koma skill ndiyatonse!
Game ndikumakana ndiyetsela ndimakako
Kufuna kundisuntha ndeyetsela ndimakako
Sikamadza kokha
Ine ndiwakunyanja ntchito yanga ndimakoka
Koma ndikasanja zima babe ndimakako
Ndipo sindimafooka
Pa top osachoka
Ndakulandani joker inu ndi ana anjoka
Beat yi ndi Diva ndimaikwelakwela
Sikuyamba kuipha imandifelafela
Ndikuyamba kundimva?uzindimvelamvela
Ma babe amandifeela ngat tima aluvela
Ndinakwatila beat ndimakhala ku stu ndukhala pachikamwini
Ndinapachika nkhawa anadzipachika mwini
Ngati mtengo Wa Gwafa pa beat ndimatelela
Ineyo ndi machine ma truck ndi ma telela
Uthakuona mmene nyimbozi ndimaphelela
Mwina ndili ndidziwanda nde muzindipemphelera
ndaoloka dzilumbazi
Ndimaika rap osati lumbazi
Kumveka Mangochi mpaka Lumbadzi
HEYO GD yafika yaMijombazi
Chaka chino ulaliki ndi anga ma verse
Odziwa malemba ndiomwe angamamvese
Koma ndilalikabe enawo abalalika
Ndikayamba ineyo enawo abalalika
Ena apakatika
Ena atapatika
Mafana ndimapweteka nkuwaudza zimachitika
Mumachulutsa kudzithemba
Kudzithembelela
Ena mukapsa moto chifukwa mmadzithembelera
Nawe Ace jizzy undibwenzere Yanga dollar
Collabo yachaka chatha mpaka lero osayimba
Kapena mutamvera munadziwa simulimba
Hhaa?
Kwachuluka ma guy amisomali
Amatikhomelera
Mkumatigonelera
Sindidziwonelera nane ndovuta kulela
Pa beat ndine wa umve nde mudzidwala kolela
Sangakhale fly ndatenga chokolela
Siulipo wekha mulipo kaphava
Oimba oipa okuba mbava!
vibe yako ili bho koma lyrical mbola
Umayetsa uli ndi bomba koma lilikombola
Ndimaika ma Punch umaika malido
Iwe kuimba ndine ungakhale Nkhomaliro
Tingasonkhane kwanu kungakhale maliro
kundisata ineyo ukusata imfa
Oyimba wazima tracksuit za taifa
Siumavala zodhula
Khosilo ndikudula
Kukumenya kumuutu nkusakaniza medulla
Anthu ngati inuyo chakunoko timabhula
Zovala ndikuvula
Kaujeni ndikudula
Mulibwanji ma hater koma coffee mwamwa?
Mafana owononga paliponse coffee mwamwaa!
Ineyo sindinati koma apapa ndikukamwa
Ati beat ndailuma ndikukamwa
Ngakhale muli Ng'ombe sindikudya beef ndikukama
Mumagona pa beat ife timagona pakama
Mumabwera ndimatama kuzitama
Ndimabwera ndimambama zimajudo kuchigama!
Ndimabwera ndima
PUNCH
AFTER
PUNCH
AFTER PUNCH ?