Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Malamuilowa ndaa mu gheto, awa ndi malamulo khumi amu ghetto,
1. Kusunga chinsinsi nkofunika/ kambakamba akhalira deal zikanika/ zikanika zinthu zoti zikanachitika/ osathokathoka mfana lamulo loyamba.
2. Nndani wako amakhala nzako/ ntima wa nzako mfana ndi tsidya lina-khomele-khomele zoba amakoma mmaso/ ukatembenuuka akuponyela chilaso/.
3. Zomwe zili nthumba sitikamba/ osabang'a nazo zose zina mfana shava/ bussnes ndi ma chick aise sizimvana/ akaz ambiri achulukawa iwe ndi mbava/ umapeleka zose mmaso muli gwa.
4. Chenjera ndi mfana wokupopa/ kambakamba ngagadiwa zambiri angothoka/ ngati muli pa bawa/ cholinga nkukukawa/ zambiri angothoka mfana yemweyo amadissa.
5. Nsanje pa Malawi ilibe nzake, ngati zikufwamba/ auze siizufwamba/ nkhondo ndi anasi ndiomwewo azakufwambe/ Kukufwambafwamba pamapeto mfana kape/samala mfana iwe dziko ndi la chabe/
6. Osakongozana pa chinzake, business ndi chinzake aise sizimvana/ business ndi mafrenzo sizimvana/ mapeto ndi chidani-six watsatana/
7. Dilu siimangopheduka yokha/ pamakhala mfana winawake wakathoka/ mfana wake suunganganizire ngwachikoka/ yang’ana mu crew bwino bwino muli njoka/
8. Za nkazi wako zako zako/ kaya mwayambana zisafike kwa anzako/ ndi nkazi wako nkaziyo siwa anzako/ ukapusa uzadabwa akugwidwa thako/
9. Akatchula ntengo take it easy, ndooyambila/ kakamila atsitsila/ ugula half price/ imeneyo ndi ghetto price/ ngati uufuna kuphetsa ngini usaphetse ghetto, pita kwinako you’ll get the double price/
10. Lamulo lofunika kuposa onse, lamulo loyamba lotsiriza zolamula, opa JAH! JAH! ika JAH! patsogolo/ opanda JAH! JAH! iwe palibe tsogolo/ tsogoza JAH! JAH!, JAH! JAH! patsogolo.
HOOK
Malamulowa ndamu ghetto (ghetto)
Malamulo khumi amu ghetto (ghetto)
Malamulowa ndamughetto, awa ndi malamulo khumi amu ghetto (ghetto)