Nonymous - Kupepesa
Name of album : Kupepesa Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Ndikonda zomwe ukonda
Kodi wekha sudziwa
Ndikonda kukhala pafupi nawe
Suona chikondi mmaso mwanga
Ndikonda kuchita zonse undiuza
Zonse unena nthudi ndichita
Ndikupepesa pa zonse zomwe ndinachita
Ndikupepesa pa zonse zomwe nakulakwiira
Ndikupepesa pokunamiza kuswa mtima wako
Ndikupepesa pokhala mkazi yemwe sunafune
Ndipanga chilichose kut ndiloweso mmalo
Ndipanga chilichose
Kuti ndiloweso malo
Chikond chako nnaseweretsa
U opened the door yes
I did shut it
Ndmkaonangat am e clever one
Leaving u like that
Leaving u stranded koma ndazindikiraa
Aaaaaa
Ndazindikira aaaaaa
Aaaaaaaa aw
Aaaaaaaa aw
Ndikupepesa pa zonse zomwe ndinachita
Ndikupepesa pa zonse zomwe nnakulakwira
Ndikupepesa pokunamiza kuswa mtima wako
Ndikupepesa pomkhala mkaz yomwe suna
fune
Ndipanga chilichose kut ndiloweso malo
Ndipanga chilichose kut nd loweso malo