Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Intro:
Blakjak,,, Inde! Mavuto, Ukutinyoza (Ukutinyoza?) Iwe ndiwe M'bale wa ifetu, Okay? Lets go..
Verse1
Mkwiyo wako wandipangitsa kumakutalikira
Nkhawa yanga, sukundiuza chomwe ndakulakwira
Ukumauza anthu ambiri ukundikayikira
Kuti mkazi wako uja ndikumuzembelera
Mavuto- waiwala komwe tikuchokera?
Mkazi wakoyu si ine ndemwe n'dakugwilira?
Of coz one day ankandisekelera
but me didnt do nothing n'nali ntaledzera
Chorus
Ndayamba kale kukuyitana koma sukundiyankha
Ndayamba kale kukuyitana koma sukuvomera
Kodi nchani chenicheni chomwe n'dakulakwira
Ngati n'dakulakwira, bwanji osandimasula?
Chorus2
M'bale wanga mavuto-ziiiii
M'bale wanga Mavu- ziiiiii *4
Verse2
Chomwe udziwe chibalechi chili ngati fupa
Pena zimayenda boo, pena zimashupha
Olo palibe moto utsi utha kufuka
Takumbukira tikuvina Lupupa-Lupupa
Haha- kuchipindako tatuluka
Tiyeko tikamuone Francis Kaphuka
Tamakhalani ngati munagera pa Kaphuka
Tasekelerani, Misonziyo Pukuta.
Chorus1
Chorus2
Verse3
Zili bwinotu apa mmene tili limodzimu
Osati kumangokwiya ngati za mizimu
Aliyense akungokamba za ife mmuzimu
Akuti tikumamwa mowa ngati opanda nzimu
Naye Mkazi wako uja walowa chisawawa
Mfana aliyense otchuka n'taleka ntalawa
Mma Facebook mmenemu fanz ikumunjoya
And she is telling everyone ati samakusowa
Chorus1
Chorus2
Bridge
A wah dis me ah hear?
Unuh talk 'bot me ah nyam yoh Empress deh?
Ah why so? Cya a hug up, we ah hug up?
Mavuto- Rudebwai, Get yuh Life deh
Chorus1
Churos2
(song ends with beat)