Mascot - Kodi Bwanji (Prod by BFB and MBJ)
Name of album : G.L.C (Good Luck Charm) Mixtape Part 2 Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile

Intro
It's your boy Mascot/
Yeah/
It's your boy Mascot/
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kodi Bwanji Nkazi Kodi aaaahh/

Hook
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
(Kodi Bwanji)
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/
Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/

Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
(Kodi Bwanji)
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/
Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/

Verse 1
Kukonda kugwiragwira dollar ngati bank teller/
Mpakana dollar zanga zonse wandithera/
Sitingatchile bhobho basi undipemphe mayunitsi/
Uli tabwera tikumane pa lunch tikadye Kips/

Zandilaka wachulukitsa ma demand/
Sungandibele ndikuona you know am not blind/
Day light robbery ndiyomwe ukupangayi/
When ever I go broke ukuvaitsananso ndi mzangayi/

Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/
Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/
Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/
Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/

Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/
(Uzibwenza)
Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/
(Ndikumeza)
Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/
(Whaaattt!!!)
Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/

Hook
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
(Kodi Bwanji)
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/
Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/

Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
(Kodi Bwanji)
Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/
Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/
Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/

Verse 2

Ndikanakhala mfana wa mphwiyo bwenzi ndikunvetsa/
Koma ndine kapolo ndimachitila kukhetsa/
Thukuta/
Kuti ndipeze dollar zimavuta/
Nkapeza Ka grand nde kuti mfana ndaswetha/

Sendera pafupi umve chinsisi/
Ndine mfana wokhwima wamitsitsi/
Kadola kangako ukapanda kukabwenza/
Nkulumbira ine apa ndikulodza Aaaah!!/