34802Downloads
Trap Squad - Undifufuze
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Anthu ambiri amakuseka
Ndidziwa mtima wako umapweteka
Anthu akwanu amakunena
Ndidziwa azimzako ambiri amakunyoza iwe
Zambiri umazimva, zoona umazimvazo
Koma ndine munthu am not perfect ndimalakwaso
Mbiri yanga angayidese bwanji u'll always be my baby
Well listeni mi nah care wah dem seh coz am down for you baby.
Chorus..... Ngat simunayimvele kayipezeni pa Malawi music ilimbweeeee guyz...