2 Street - Kwacha Spender ft Kelzin
Name of album : Songs By 2 Street Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Sindikuti ndifa mawa, koma papsya tong'ola poti suziwa mtima wa ndalama
Ndiye ndikazipeza pompo ndimazi spender
Sindidikira kuti mawa kapena kuti kucha bwanji
Poti sinziwa za mawa kuti kapena kudza bwanji
Choncho mwina ndingazafe ndalama yanga ili mthumba "NO!"

Chorus


Umangoziwiratu iwe!
Kuti ya ine ija (ija)
Dollar siigona mthumba (siikhalitsa)
Ikagona mthumba ndalama imeneyo ndi haraam (malodza)