Tanaka - Tidziwe Multiplication ft V.I.C, Hamjee , Khoh Gomzy (Prod. khoh Gomzy)
Name of album : Tidziwe Multiplication Genre :Fusion
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Tidziwe Multiplication

Tiyeni tonse, tidziwe multi, multiplication
×1 (by Tanaka)
Tiyeni tonse tiroweze multiplication table, tiroweze multiplication table
Double!
×2 (by Tanaka & STD4 learners)
Multiplication ingakukankhireni kwakuya
Maso pa tsogolo, maso pa tsogolo
Munga pange zazikuru, yeah
Triple!
×3 (By STD8 learner)

Rap part
Ndakana ulesi
Ati ndi sukulu sizigwirizana mmesa
Nde pofuna kulemba masamu
Kuwonera kuchikuto daily
Kapena ndingo kopera after Mary?
Kukanika kuloweza multiplication table?
From the beginning to the end of the term
Yesera mbaliyako the teacher is not to blame
Pena zimavuta eeh! Pull up your sock eyes on school school!
Zomasolver solvers ndani adayambitsa?
Adalimbitsa moyo pena zimandi dwalitsa
Eh ndipatse calculator
Vuto ndipamayeso adzandi landa a invigilator
Bola ndingo loweza kanyimboka basi
Ndikapempha ku Domasi kakhale msilabasi, yeah

×4 (by Hamjee)
Multiplication ndimaziko a masamu, yeah
Nambala yayiliyonse
0 kapena 5!
×5 (VIC)

×6 (by Hamjee & Lucia)
Multi, multiplication
Osa gonja!
×7 (by Yui)
×8 (by Yu)

Ngati muroweza multiplication, muthakuphunzitsa ena, kulimbikitsa ena
×9 (by Yui & Yu & STD4 learners)
Ok,
×10 (by VIC)
Tiroweze, tiroweze, ka nyimbo ka tiroweze
×11 (by Yui)
×12 (by Yu)
Tiroweze multiplication table, kunyumba kusukulu kulikonse, kulikonse, kulikonse, kulikonse
Tiyeni tonse, tidziwe multiplication