Mr Mzaliwa - Basi (Prod. Dry B & Me Qelito)
Name of album : Basi Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


[INTRO]
It’s a king Wa Malawi oohyeah..!! /
Mr Ayaya..!!!
(Verse 1)
Ukamwetulira mtimawu /
Dhu-Dhu kugunda /
Ukasekelera nthupili /
Paliponse kukoma /
You look so credible /
You the one I love /
Para nakusowa vikwenda yayi /
Darling ndiwe moyo wa ine /
Ukatalikira ndi madwala /
Nkhukupenjanga mazuwa yonse /
Mawazo ikundivuta /
Ndakumising’a masiku onse /
Ndiwe provider /
Ndiwe chitetezo cha ine /
Undipatse mpata /
Ndikukonde mpaka mapeto /

[HOOK]
Tenga zanga zonse basi
…!!!
Pa iwe ine ndathera
Ndiwe nthiti yanga basi
…!!!
Pa iwe ine ndafika
Umandikonderamo
…!!!
Usamasowe
– usamasowe
Umandikonderamo
…!!!
Usamasowe
– usamasowe

(Verse 2)
Ungasowanga yaye
/ Ishi na mimi / Uwenge nane / Niwewe pekee /
Ndimafuna love ya kanthinthi / Yosawona nyengo / Undisambizye mwantinti / Mopanda zilango / [HOOK] Tenga zanga zonse basi…!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi…!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe (Verse 3) Zomwe ine ndinkakhumba / Ndazipeza zili mwa iwe / Aka ndi kanga kanga / Palibeso oposa iwe / Zafika ndikuthangatire babe / Bwera kuno ndikunyadire / Zikavuta usandilalatire hunie / Mwachikondi undilakhule / Wewe ni mwanga / Katika maisha yangu /
Ninakuhitaji kila siku / Wewe ni moyo wangu / Unanipa furaha hata / Ukiwa mbali / Kulikonse tingapite apa / Tili awiri /

[HOOK]
Tenga zanga zonse basi…!!!
Pa iwe ine ndathera
Ndiwe nthiti yanga basi…!!!
Pa iwe ine ndafika
Umandikonderamo…!!!
Usamasowe – usamasowe
Umandikonderamo…!!!
Usamasowe – usamasowe

[HOOK]
Tenga zanga zonse basi…!!!
Pa iwe ine ndathera
Ndiwe nthiti yanga basi…!!!
Pa iwe ine ndafika
Umandikonderamo…!!!
Usamasowe – usamasowe
Umandikonderamo…!!!
Usamasowe – usamasowe