Click here to download this song >> Desktop | Mobile
INTRO--pachimkwezamau basi,,,
kamodzi kawili,,ah king chambiecco
Kachikena,,abwere adona awo,,eeeiii,,eeeehe!!
CHORUS--
-pakamodzi Ubwere n'dzakuoneko
-pakamodzi ubwere n'dzakukondeko
-pakamodzi ubwere n'dzakugwireko
-pakamodzi ubwere n'dzakupyontheko,,n'dzakuoneko,,n'dzakugwireko
-Paka Paka Pa Pakamodzi
--ubwere n'dzakugwireko
--pakamodzi ubwere n'dzakukondeko
--pakamodzi ubwere n'dzakuoneko
--pakamodzi ubwere n'dzakupyontheko
--pakamodzi ubwere n'dzakugwireko,,n'dzakuoneko
--Paka Paka Pakamodzi
VERSE 1
-ndungofuna ntakuonako
-ngungosowa ntendere ndikugonako
-ubwere ufulumire n'dzakupyontheko,,n'dzakupapaseko,,n'dzakukondeko eeeei
-timambama n'dzakumenyeko
-zachikondi zosisita zokutsinako
-kumashobi nkukutengako
-nkuzagula zitumbuwa nkukumanako
-kuzandithamangitsa iwe nkundigwirako
-mwachikondi iweyo nkundifusako
-daaaaarlin,,simundipatsako
-hahahaha,,ine nkuzanyemako
-zosewera zachikondi ka ubwanako
-nchewa nkuzazimva ka ubwanako
-kuzakugwira kukumbata nkundikanako
-tchetera lachikondi nkuzasekako
-kuzakukoka timasaya nkukudinako
-choooooka!!!! Tima-Dimples timakhala chonchi iwe
(Back to chorus)
VERSE 2
-mubwere panyumba adona heeee
-moyowu sukukoma ndekhandekha heeee
-chilichonse chasiya kukoma heeee
-ubwere ndidzadye zo_baker iweeee
-zachikhathu zosapsa nkunonabeeee
-kukanika kukalipa nkudekha ineeee
--aaaaaaahaaaa!!!!!!
-ndufuna ntakuona ineee
-ndatopa ndekhandekha chiyenda yekha inee
-ndazisowa zako zija zomeka weee
-zovala zothina zosalalitsa iweee
-weekend nyakula chilundu iweee
-ine pakhonde manja nkhongo nsunamo nduu
-kuganiza ndikuona liti mama weee
-ukumandiimbitsa tinyimbo ya ya yeee!!
-oooh na na na na na na na naah naah eeeeiiiiii
-kamodzi kawili ah king chambiecco pachimkwezamau kaya zumvekaaa!! Mubwere adona inu
(Back to chorus then repeat verse one)