Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Sindidzaku khumudwitsa ayi (Ndiwe Wanga Iwe)
Ine ndidzakukonda iwe
Ngakhale wina andinene ndiwe ndasankha
Kulikonse ndidzapite nawe udzanka
Namalenga pemphelo lijano wayankha
Mkazi ndiwe wanga, nena inde
Sindzaku khumudwitsa ayi (ndiwe wanga iwe)
Mkazi ndidza kukonda iwe
Monga madzi ozizira
Kum'mero kwa yemwe ali ndi ludzu
Iwetu ndimaku dalila
Ndiwe Koloboli ndine chikhudzu
Apasula mamvera-mvera
Wachitatu njoka muudzu
Mkazi ndidzakusamalira
Kukutonthoza ukamalira
Verse 2
Ndikufuna kukhala nawe muchikondi
Ndiku khulupira ukumva siiwe gonthi
Mkazi ndikufuna tidzipanga chonchi
Wachitatu ndiwosokoneza moti
Momwe ulilimu sindingamenye ndichikoti
Ayi, olo khofi indedi mpaka mdothi
Ndidzakupatsa chikondi udzati abuna ali ndi muti
Ndikakoti zwee! udziti abuna ali kuti
Chikondi cha daily, ayi chopanda tchuti
Monga msilikali, tsiku lonse kubeleka mfuti
Unifolomu ya chikondi, kumapaziku bhuti
Ndipamene iwe udzazindikile zoti