Odick - Swazi
Name of album : Voice of The Voiceless Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO
Haaaaa! Swazilicious Odick! HAHAHAHAH!!!!!
Ndakumana ndi Jane dzulo koma ngati andimanga ma chain,
ine kufuna kulowa pansi  Ndinchaka amanditcha!!!

HOOK


Amanditcha swazi ,ama! Amanditcha swazi!
Zamababie sindimatha n’chaka amanditcha swazi!
ama! Amanditcha swazi!x2, Zamababie sindimatha
n’chaka amanditcha swazi, Ndimafuna, (nditakhala Nswati)x2
Ma Babie anandilaka n’chaka amanditcha swazi!
ama! Amanditcha swazi!x2, Zamababie sindimatha
n’chaka amanditcha swazi!

 


VERSE ONE


Ndine Robort,Cyborg infact ndine swazi
Ndikavaila ma hope okha amangonditcha blazi
Akazi omwe ndavaila akhoza kukwana track
Mababie amandikana ati ndine wachi tradi
Man thokani zina zama babiezi mayazi
Kuthoka ndimafuna koma munthune manyazi
Mu class yama swazi amanditcha kuti Ngawzi
Amanditcha swazi zinalina wansembe! (BRIDGE)
Mfana ochibanda wamalooks ngati wa reggae
Am not that handsome but am so sexy,
Ndine swazi wa default ma babie anandilaka,
Mu level yama swazi am lapping up the ladder!
Chick ikandikana ndimapeleka ma khatcha!
Ma chick amasiku ano amangofuna ma kwacha!
Amafuna Blackberry, House, Car komanso Mphasha!
Ndimangoti kagwele uko kulibwino nzafe Bachelor!

 


(HOOK)


 


VERSE TWO


Amanditcha swazi, mdani wachi terminator,
Ndine swazi akazi kwa ine ndima predator.
U can’t seduce me coz ama go-getter,
Ndikusopasopa nga-ngati m’bulu wa yogeter.
Ndine swazi!  zinalina mfana wazipika
Chick ikandijaila ndimaiwuza zipita!
Mental ikabeba sindisiya ndima spita
Mababie ali mbwee! Koma mfanayo ndiouma basi!
Mfana osatopa 90 minute ndingo warmer basi! (Kubunyula)
Ndine ouma gwa! Ngati actor wa war bus!
Zamiyendo iwiri sindimadya ndikunenatu Mathanzi!
Mababie akuti sindimato-to-to-to tha zinthuzi
Papalazi busy on the line kundito-to-tola Zithuzi!
Kukanidwa ndi Chick kwaineyo man sinkhani
Chick ikandilola madoro amangobwela ndiphazi
Zikamatero choncho ndiye mukuganiza ine ndingatani?

 


(HOOK)


 


VERSE THREE


A wanna  have Akazi five ngati Zuma
NDIYE BVUTO NDI CHANI? Ati akazi amaluma!
Am so rigid ngati Nsomba yodumwa!
Ndine mfana ouma gwa AKA kwale
HIV ili kutali ine sindingadwale,
Zachibwenzi mayazi tizangopeza Chick ndi marry!
Or ndizagwila miss Malawi Faith Chibale!
Ndinayamba ku hopela ndili ku Nusery,
Mpaka chickyo inagwidwa tli ku Secondary,
Pano ku college koma ku hopela ku primary!
Oh-Hooo! I don’t think am normal!
I know! kukhala ndi Chick ndizikhomo!
Ngati uli Swazi zimangofuna kubvomeleza!
Kunama kuti uli nayo Chick ndie kusokoneza!
Just be patient maybe uzabooleza!
40 years opanda Chick man mwandifooketsa!

HOOK X3


THE -END