Trap Squad - Waku Blantyre
Name of album : Family Over Everything Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Verse 1(Chavura)


Mu b town ndimafila life (LIFE)


Aliyense oyimba ndi ine ndimakiller guys (GUYS)


Ndikamalemba verse ndimatcheka line up (UP)


Kuyisiya fans m'madzi ngati pine appl'


Ndimazisata amathoka shit (SHIT)


Amasata nkhani zanga ndikasoka chick (CHICK)


Mafanawa pa internet amandistokadi


Akandipeza amandifunsa, amandibowadi


Zowonadinso mafanawa simachita show (SHOW)


Ronald'nso nyimbo zawo samamixer bho (BHO)


Tawonaninso achina volver amangoakhilanso


Amafuna atandibula ngati filabo


Pozandibula azafila bho (BHO)


Ngati chick yopanda mbina sazachithako(KO)


Chino ndichiakita mfana sazachiphako(KO)


Wake ndadya koma wanga sazachi... ha


 


Chorus(Stich fray)


(Kuyenda


ntown) aliyense maso pa ine,amene


samandiziwa angoti uje bwanji


 


(Ndiyende ntown) aliyense maso pa


ine,amene samandidziwa angoti uje


bwanji


Amene amandiziwa akuti ndine DOLO


Amene amandiziwa akuti ndine SHASHA


Amene amandiziwa akuti ndine DOLO


Amandifila fukwa ndine waku blantyre


 


Verse 2(Revolver)


Akuti volver timakufila ku mponela


Nyimbo zanyuwanizo muzitiponyela


Achina mbina mbina muziti ponyela


Ndikutentha mahater sakuwothela


Amanditcha austin, mfana wa powers


Osati movie, ndikuthoka za bawazi


Green ndimamwa, mu tracks ndimamudya


Akuti ndi mfumu komabe ndimamuda


Get it, musamude fumu-lani


Stich andifunsa 'iwe volver uku-tani


Zomapanga beef suzatukuka nazo


Olo utahitter sakutenga kuma show'


Neighbour wanga akuboweka


Sandiziwa koma nyimbo zanga akuloweza


Speakers on blast, chifisi pa repeat


Ine nditachokapo kubwela round six


(chorus)


 


Verse 3 (Stich fray)


yeah,them wan fi follow me ina real


life


But mi so tweeter me forget & mi


nah follow back


Amati hater koma


chonsecho amatifila


Ngati ma chick awo athetsa amatilira


Check it afuna


khalangati ifedi,


Kuzimva u landlord mu


gameyi koma ali pa rent (HA HA HA HA)


,


ndima students ozimva u head,


Ratatatatatata,stichfray ndinedi


Ndinedi DOLO


Amene amandiziwa akuti ndine SHASHA


Amene amandiziwa akuti ndine DOLO


Mukut


sim'mandiziwa pamene ndimakubowani


(chorus 2x)