1788Downloads
ABC - Ndine
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
ndikakhala zimandivetsa chisoni/
ndenkha manyazi amandipeza kuti ndikupatse moni/
poti ndine munthu oipa kwambiri/
poti unafunitsitsa kuti tizakhale awiri/
ndine amene anawina mtima wako/
poti ndine amene umanyada naye kwa anzako/
umati uli ndine wapamtima pako/
koma ndine amene makusewera chipako/
panali ambili amakufuna koma umati uli ndine/
za akwanu sumava zoti tisiyane iwe ndine/
ndinachongetsa aliyese amaziwa/
unalinane pali pose zachibwana umapewa/
koma ndine olakwitsa kwabasi/
ndimakonda akazi/
ndinakuswera mtima/
you didn't believe it utandipeza ndi wina/
kupepesa ndikwanga, munthu amalakwitsa imva mau anga/
ngakhale bho sunayankha, unasithilatu mawanga/
tipange chimodzi/
pano madzi ali nkhosi/
tizakhale limodzi/
iwe ndine pamodzi/
chorus
ndine ndinayambitsa ndine/
ndinakuswera mtima/
zinthu zako zinaima/
koma chomwe ndikupepha ine ndi mwai wina/
poti zosezi ndine/
ndinalakwitsa ndine/
ndikupepesa ndine
ndine ×2
tibwelerane iwe ndine
verse 2
pano umati sungakonde mamuna/
unalumidwa ndi chakuda/
koma chomwe ndikupepha ndi mwai wina/
ngakhale pano umandida/
when am texting you umachulutsa ma delays/
koma ndine to make you kundipewa nowadays/
undipangitsa ndidwale/
koma zakale uiwale/
mpaka kale tizakhale/
ana tizabale/
tizathandize achibale/
tsogolo lanthu lizawale/
ndikudikila yankho lako/
dziwa ndine nthiti yako/
bambo wa ana ako/
ndikufuna kukhululuka kwako/
unalinane palipose kulikose limodzi/
mkakumbuka zanthu zose chilichose pamodzi/
am begging you ndipatse mwai wina/
tizapange zina/
tizakhale limodzi/
iwe ndine pamodzi/
no one plans to make a mistake/
but it's a mistake to repeat a mistake/
chorus