Dapa - Ndipatse Mpata (Feat Blaze)
Name of album : Issuez II Genre :RnB
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Ndikufuna mtima wako
Ndatopa ndizoti ndizingokhala n`zako
I can neva be your friend
Ngati ufuna ukhale zose wachikondi and your friend
N`kale n`nayamba kufusila
Nanga bwanji umangondiyika pa hold
Ndalephela kupirila tangonena zomwe ukufuna ndipange chani kodi??

Ndakumana ndizokhoma
Kufunsila kumangowomba khoma
Zili mtsogolo zokoma
Sindifooka ndiwe amene ndimafuna
Alipo mpweche matsuna
Koma sindufuna kugwela n`mbuna
Poti enawa amangosaka chuma
Sindugona ndungopanga phuma!!!!!

CHORUS
Ukangondipatsa nthawi iweee                    x2
Uzasiyanitsa iwe
Ukangondipasa mwawi iweee
Ndizagwilitsitsa ineee

Mpatse mpata pata pata pata pata pata pata pata pa gal           x2
Mpatse mpata pata pata pata pata pata pata pata pa yeahhhh

VERSE 2
I promise you am gona show you better love (better love)
Chikondi chomwe suudawone since you ever loved (Ever loved)
A lot galz out there
Komabe mtima wanga wasankha iwe
Kodi wekha suungadabwe
Chifukwa chanu nkumakakamila iwe?

Lem prove it to youuuuuu
I dnt wana play games
Ndiwe mtima wanga watengaaaah
When am dreaming its youuu
Ndakana other names
Iwe ndine mpaka ifa ndiyomwe idzatengaaaah

CHORUS