80315Downloads
Kalawe - Dzuka Malawi (Remix) ft Fredokiss, Martse, Mwanache
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
OLO ASINTHE THENGO ,AMAKHALABE FISI/
OLO MFANA WAKE AMAZAKHALABE FISI/
TINKANENA UJA LERO AUTHELA MU SIZI/
JZU ANATHOKA
MULTIPARTY KNONDO/
YOPANDA MIKONDO/
KNHONDO YA MIZIMU
YA MAGANIZIDWE
NKHONDO YA UMPHAWI
ETI UKO WANTCHITO WAWO AMAMVINILA/
AKAAMAAPHIKILA AMAMUVINILA/
AKAMAPAKULA, AMAMUVINIILA/
PAMAPETO AKE ETI AMAMULIPILA/
AM SWIMMING SO DEEP LET ME GO ALITTLE SHALOW/
NKHONDO YA MIPENI TUUVUNGA ZIBALOBALO/
MMBURUNDI KUTSEGULA OKALA ISANDUKA WHOLESALE/
MMALAWI KUTSEGULA WHOLE SALE ISANDUUKA OKALA/
AWO ANABA DOLLAR, TINAAVOTERABE/
UYU AKUBA LERO ,TIZAMUVOTERABE/
KUNJAKUTU KWACHA KOMA UKUTYOLERABE/
ANANSHUTA MPHWIYO NDANI?/
CHIFUKWA CHANI?/
GALIMOTO LA NJAUNJE ANAOTCHA NDANI?/
NOTHING IS IMPOSSIBLE/
YESU ANANDZUTSA LAZAROTU ATADIWA/
NSINGA ZA NKONONO PA IWEO ZAMANGIDWA/
JAH PATSOGOLO NSINGAZO ZIMASULIDWA/
JAH PATSOGOLO TIDZUTSANA MMODZI MMODZI
DZUUKA!!!!