Phyzix - Chi Nyimbo ft Gwamba, Martse and Emm Q
Name of album : Gamba Wa Suit Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Verse 1 by Gwamba Koma ase Gwamba uja ase amatha kwambiri/ ndinkaona ngati verse amalemba masiku awiri/ amangolemba pompo eti, mfanauja ndi teacher/' amatero ma rappers wa akandipanga feature/ 'koma cha penapake Gwamba uja amatizunza/ tiziti zonse timakambazi sizimukhudza/ atangoyankhako tikhoza kutchukabe at least/' amatero makape ndikapanda kuyankha beef/ beats ndimayidwa mafana amangowoma/ ma punchline anga ndinachongetsa ku cosoma/ ndikamakwera mental, ndimasintha ma style, ndimangosinthabe mpaka fans imve kukoma/ ine ndine chimbuli chimbuli chopanda tchuzi/ ndikumakanika kunena spelling ya maluzi/ ndikumakanika kunena spelling ya ukape/ ndikumakanika kunena spelling ya ubate/ haaaa! Verse 2 by Phyzix Nkhawa zanga zonse ndinamwela mowa/ ndimasaka ndalama nchifukwa ndinasowa// Pakali panopo nde ndibowa nyimbo zanga pali ponsepo zipezekapo/ Siiine munthu wamba ndaimba zaka zingapo/ ngati sumandidziwa ukafunse amako/ / pa banja pa chimzake pa chibwenzi / Nkhani zimakambidwa ndi za/ mani phyzi/ x / mfana wa matsitsitsi ndekuti ndimabhawika wa mu botolo Ndimatha kwambiri umenewo nde u phyzo wo/ omwe munandisowa tikumane ku show/ Ndimatha kusiya kuimba ndikubanduka/ ndikafuna kuyambilanso nyimbo nkutchuka// Ndinayamba kale kwambiri zimenezi Palibe angandipusitse zoyimbayimbaz