3267Downloads
Don Foxxy - Wake Up Malawi
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Step up recordz!!
(Dzuka Malawi dzuka) uuuuu aaaa eeeh
(Dzuka Malawi dzuka) uuuuu aaaa
Chorus
Malawi the warm heart of Africa ooooh yeeee X2
Wake up Malawi
Wake up Malawi eyaaa
Wake up Malawi uuuu
Wake up Malawi oooh
Verse one
Dziko lathu olitukula si president ayiii
Koma machitidwe athu ndi omwe akuononga dzikoli iii mmm
Katangale ,dyera, kudzikundikira chuma eyiii
Moyo odalira osafuna kulimbikiraaa ooowoo
Dziko litukuka bwanji ngati athu akungosewera bawo? mmm
Dziko litukuka bwanj ngati anthu akungodalira kulandira? eee
Ayeeee eeee wake up Malawi mmm
Ayeeee eeee wake up Malaaaaa wi iii
Chorus
Bridge
(Dzuka Malawi dzuka) x2
Mmmmmm mmmmm
Verse two
Tili nawo anthu andalama zankhani nkhanii ii ooooh
Omwe atha kukwanitsa kutsegula ma business ii iiii
Ena mkupatako ntchito, Kwinaku nawo akukatamuka
Koma ayi safuna ndalama zawo n’zamanyado basiii iii yeee
Achinyamata kumasauka zochita akuzionaaaa eee
Ati zochosa swaggie, sangachite kuopa kunyozeka kwa ma babie
Zitheka bwanji dziko kukhala wathu ndalama wa amwenye? aaaaa
Wake up Malawi uuuu
Wake up Malawi
Dziko lathu silosauka osauka ndimaganizidwe awanthu
Dziko lathu silaumphawi awumphawi ndimaganizidwe awanthu
Wake up Malawi choncho
Wake up Malawi yeaah
Wake up Malawi
Wake up Malawi yeee
Chorus