11812Downloads
Gaspa - Udzasimba feat Saint [Prod. Gaffar & Snics]
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Ndati ndikuwuze love yanga ndiyolimba
Utha kundikana siku lina udzasimba
Tangondilora uchilawe cha bad man
Tapanga zotheka usachuluse makani mayi
Ndikulonjeza ine sinzakudabula
Chikondi ndilinacho chinazaza chitambula
Just give me the keys let me enter in your heart
Singavayire wina you my number one chart
Chimene ndikufuna nkazi undimveke mphete
Ndikutengele pena ma hater akhale chete
Daily ndikavayira umagwanda ngati chakwamba
Tandipase mita love yanga ndiyosayamba
I can be that guy kanyamata kosamba
Tachiyese wekha ndisachuluse zokamba
I can be that guy kanyamata kosamba tachiyese wekha ndisachuluse zokamba
CHORUS
Pano utha kumandikana kanekane!
Chifukwa sumandiziwaaa
Utha kumayelekedwa
Yelekwede!
Chifukwa sumandifiraaa
Koma ukazangondilora
Udzasimba iweeee *2
Koma ukazangondiziwa
Udzasimba iwee*2
Zachikondi cha ineee!!
VERSE2
Zoti ndimakukhumba bwino bwino umayada
Koma ndikavayira nanga bwanji umanyada
Iwe tandilore suzapangaso regret
Love yanga ndiyambiri ndikugayira chi plate
Tizakhala limozi kulikose tizayenda
No sonye koma kwacha tizasipenda
Nanga bwanji umafuna nzikunyengelera
Kapena umafuna kuti ndizikupemphelera
Koma nkazi tasegula chikhomo
Sendela pafupi tandipaseko milomo
Be my main chick wanna take you to jameka
Chilichose ndikwanisa tangopanga zotheka
Zachikondi changa palipose fusafusa
Ngati maliro mlaka umandidusadusa
Zachikondi changa palipose fusafusa
Ngati maliro mlaka umandidusadusa
CHORUS BACK
PRE-VERSE
nanga bwanji umapwetekesatekesa ngati pachilonda
Nanga nzanenenene bwanji zoti ndimakukonda
Umangophwekesa phwekesa
Umangochepesachepesa
Ngati udzalesesalesesa zachikondi cha ineee!!