Don Foxxy - Zibwana
Name of album : Zibwana Genre :Local
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Chorus
Anyamata amasiku ano zibwana
Dzibwana  eeee dzibwana
( too much Children)
Anyamata amasiku ano dzibwana
Anyamata amasiku ano dzibwana
Dzibwana  eeee dzibwana
( you not grow up doing things like children all times)
Anyamata amasiku ano dzibwana

Verse 0ne
Amayi akuti steni
Abambo akuti m’dala
Dzibwana eee dzibwanaaaaaa
Azakhali akuti mtizi
Amalume akuti mkozi
Dzibwana izi nzibwana
zovala akuti swaga
Ena mkumati ung’ono ung’ono
Dzibwana eee nzibwana  iiii

Chorus


Verse Two
Akumayenda matako pamtunda
Kumati aoneratu lil wayneiiiii
Ife tikadzudzula akuti mtradi
Sitayilo yometa akuti mohoku
Kuyimba nyimboku akuti kumanza sound
Akafuna kuyankhula ndimakolo
Aaa big maninso trogi mwandishopherayi
Ndiye sikundiwaza olo mpang’ono 
Zimataxi chonchi ngati matrogi ovala atumiki
Timafunan ung’ono ung’ono  wina wake waboo ma flat