Atoht Manje - Liti
Name of album : Singles Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Verse 1...
Ogwira ntchito m'boma angochulutsa drama/
Akumangotinamiza nkumatibela ndalama/
That's why pano tili ndi economic trauma/
Tikawafunsa akumabwera ndima big grammar/
Nkhaniyi ndikhoza kuuza obama/
Akanakhala moyo nkanauza osama/
Mwina akanabwera ndi mabomba kapena kuzawaza mapama alright then.....
Nde mnanji iwe local farmer/
Mbeu zako mitengo amawaza ngat mbama/
Kukhala ngati kulimaku sikumafuna khamaaa khamaaa oh yeah yeah...
Chorus...
Akuti tizagula hummer, Liti?
Tizamwaza ndalama, Liti?
Akuti tizakhala tikuyenda chokhala. Koma liti? Mpaka liti koma liti..
Akuti zinthu zizasintha, liti?
Akuti sazabanso ndalama, liti koma liti mpaka liti..
‪#‎Verse‬....2
Nkaona amasiye pano akungosafala/
Ali balala balala mu gheto kumachita kusowa zovala/
Inu muli nawo ambiri makopala /
Bwanji osawapatsa ka hands akagule kaphala yeah.../
Nkaona olumala ambiri akungopondelezedwa/
Zaufulu wawo pano akungonamizidwa/
Akati apemphe ngongole pano akungokanizidwa..
Yeah pano angothamangitsidwaaaa....
Nkhaniyi ndikhoza kuuza obama/
Akanakhala moyo nkanauza osama/
Mwina akanabwera ndimabomba kapena kuzawaza mapama ku Capital hill rrrrrrrhhhh...
Zinazo mumva mommo
Back to Chorus...