KYC Nyimbo - Machesi (prod. Malde beats & Red Disc Music)
Name of album : Singles Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileMACHESI LYRICS VERSE 1 Geli ndinamaliza timapepala ndili nato/ Inde school siimatha koma tilipobe tingapo/ Toti nkanati ndili ku dziko lina lakutali/ Tikanagwira ntchito koma osati ku Malawi/ Mdala vep inaima, ndi steniso divorce/ Pano anabalalika sitimashala limodzi/ Its been a couple of years now since I heard his voice/ Ndango-ganiza zongoiwala ndilibe choice/ My life is on fire, palibe ondiphula/ Singagweso mchikondi akazi aku Malawi anadula/ Ghetto yut alibe kwacha, akazi amamuthawa/ Akasangalala ndekuti wamwa ka bawa/ Chifukwa chomwe navaira ku geli sinduchiona/ Ndipanga bwanji inspire ana omwe akundiona/ Nde after kuboweka, ndinapanga chisankho/ Pano ndimangoyaka poti dziko ndila tsankho/ BRIDGE Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/ Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/ CHORUS Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/ Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/ Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/ Mechesi, machesi, machesi VERSE 2 Kukhala ku Malawi, ndikulimba mtima / Kuli anthu ikutha week osaona mbamu ya nsima/ Sindili pa ufulu ngati nthumba mulibe dollar/ Dollar za msonkho wanga wina chikwama anachitora/ Regimes do change but, things dont change / Ndimakhala ozizidwa ndi nkhanizi ngati sangie/ Am 25 I should `ve been driving my own range - rover/ I got papers koma ndine lova/ Pepani atsikana lero mbina sizisuntha/ Ndiimbe zoti mukamva ubongo wanu ukhuta/ chifukwa cha umphwawi akazi analowa mbola / utha kulandidwa lero dzulo utapheya lobola/ zimachitikazi zimandizunguza bongo/ mkona nkhawa zanga zimathera ku nkalabongo/ mfana wa degree, akungomwa nkalabongo/ after 2 years wa degree wadiwa ndi nkalabongo BRIDGE Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/ Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/ CHORUS Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/ Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/ Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/ Mechesi, machesi, machesi

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com