58227Downloads
Waxy Kay - Tsokonombwe (Prod. Crown)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Anzanga a age anga pano anakwatira//
anapeleka phaa nkazi anawanyanyalira//
anasiya geri nkuyamba ma gobo//
wez penda penda pano zikuyenda bhobho..
Anzanga ah age yanga ena Ali pa vep//
ife tikadali jobless koma sitiluza faith//
mwayi ulipobe ngat sinatipeze death//
Timangopempha jah jah ationjezele strength..
Anzanga Ena kugeri sanali magenius//
Koma pano anaiphula akuyendera ma hirux//
omwe tinkakhozafe umphawi watiyanja //
Timagulitsa Zibwente kuti tidyese banja..
ah life ndichoncho//Pena zimayenda pena kugwera kumphopho//
uzasutha one day sungangokhala pompo//
osapanga phuma zizayera opanda sopo//
Verse 2
Ungokhala ngat tsokonombweee//
utha ntunda nkudupha ndukuuza tsokonombwe/
umafuna kuphura mwachangu ulowa nazo umbanda//
yesa mahaso angapo sachezelera nyimbo imodz mganda..
Mulungu anakupasani.chuma kuti muthandize opelewedwa//
malo motithandiza mpameneso tikubeledwa//
Mdaliso wa mulungu mwasandusa chotilangira//
ndife atsokonombwe pano one day muzatigwadira
Osaiwala Kuthamanga sikufika malume//
njalezo ndizanu koma chuma ndi mbalume//
tizapaka chitosi pomwe muzatilume//
mano azavunda simuzadya nao beef yothira wa mame..
Koma...aah life ndichoncho//Pena zimayenda pena kugwera kumphopho//
uzasutha one day sungangokhala pompo//
osapanga phuma zizayera opanda sopo.