Click here to download this song >> Desktop | Mobile
CHORUS
Umandipatsa appetite
Ndiwe appetizer
Umandipatsa mphamvu zambiri
Ndiwe energizer
Umanditsitsa mtima
Ndiwe stabilizer
Umandipatsa appetite
Kantima kofuna kudya
VERSE 1
Chiyambire kukhala nawe ndikumadya zedi
Ukumandipatsa njala ndiwe Lucozade
Ndukonda kudya nyama wandiyambitsa nkhwiru
Chinangwa chokukuta ndicho fruit after meal
And its…kinda strange kudya cha mma seven
Eight, nine, ten mpaka cha mma leven
Kudya osatopa
Dzala ndikutsopa
Osanama ngini ili proper
Ndeno…ka flavor ka chikondi cha iwe… pine apple
Nde... daily chikondi change chingochita pile up
Ndi anzanga ndikunenedwa
Akuti ndikunenepa
Mmene ndudyera zuyenera kukhala choncho kumene ka
Zophika zimamveka zokazinga eti
Ngini ili bho Yes! I’m lovin’ it
Ndikakhala nawe ndiyiwala zambiri
Honey tiye tizikhala awiri
CHORUS
Umandipatsa appetite
Ndiwe appetizer
Umandipatsa mphamvu zambiri
Ndiwe energizer
Umanditsitsa mtima
Ndiwe stabilizer
Umandipatsa appetite
Kantima kofuna kudya
VERSE 2
Sinkuyang’ana za diet ndingodya, mphwa ayi
Umachotsa nkhawa zanga zonse ndingomvera ire
Ndikondwa ukumbuka kuti love takes two
Chirichonse chingoyenda Ambuye mbali yathu
Nde…
Panopa kudya kwanga kwafika pa worse
Ka soda pambalipa mwina just in case
Kuntima kwangaku chimwemwe zedi
Ndithokoza kumwamba chifukwa cha iweyo babe
Nkaona nkhope yako kumva kutsekemera
Sumadabwa nthawi zina ndimangosekelera?
Mtima wako wokongola ngati umadya make up
Nde akuti ndikusiye babe sizithekatu
Paja wati ndikuvuta nkudya
Usiku cha mma 2 kudzuka nkudya
Chikondi chakochi…ngati umathira spice
Osanama darling it feels real nice
CHORUS
Umandipatsa appetite
Ndiwe appetizer
Umandipatsa mphamvu zambiri
Ndiwe energizer
Umanditsitsa mtima
Ndiwe stabilizer
Umandipatsa appetite
Kantima kofuna kudya
VERSE 3
Ndumati nkachoka podya chinanazi
Sindisiya pompo ndidyanso bananas
Zafika poti ndayamba kumana izi
Ena ati ndidya mopanda ma manners
Kudya osatopa
Dzala ndikutsopa
Ngati ili subject ndine wosadropa
Kudya osatopa
Dzala ndikutsopa
Osanama ngini ili proper
CHORUS TILL FADE