42740Downloads
Kelvin Sings - Kuyambira Lero (Prod. Dj Sley)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
VERSE 1
Ndinafatsa kulingalira ine
nkhawa inandigwila ine
madandaulo onsewa
dziwa amasautsa ntima wanga
komwe kuli kokuya
si komwe ndinaponya mbedza yanga
BRIDGE
koma ndazindikila
kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe
kundimvetsa ngati iwe
nkona ndidza kwa iwe
CHORUS
Chikondichi ndi chako chako chako
Mtimawu ndi wako wako wako
udziwe kuyambila lero
udziwe kuyambila
zonsezi ndi zako zako zako
mtimawu ndi wako wako wako
ukamagona usiku wa lero
udziwe kuyambila lero
VERSE 2
eko ntima wanga utenge
palibe wina angausamale bwino
chauta nkhawa zathu asenze
palibe wina angazichengete bwino
nde kulikonse tikafika
nyengo zathu zizasintha
koma ndiyambe nkupepesa aa
pepa dale ndinaswa ntima wako
BRIDGE
koma ndazindikila
kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe
kundimvetsa ngati iwe
nkona ndidza kwa iwe
CHORUS
Chikondichi ndi chako chako chako
Mtimawu ndi wako wako wako
udziwe kuyambila lero
udziwe kuyambila
zonsezi ndi zako zako zako
mtimawu ndi wako wako wako
ukamagona usiku wa lero
udziwe kuyambila lero