Charisma - Thila ft Donzo
Name of album : Kuntha Msinkhu EP Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileThila thila thila thila This is an awesome turn up song...And i so happen to have half the lyrics Verse 2(Donzo): Odi nkodze kaye Nsipe kaye nsilikali_ atino ndi shots on shots on shots on shots Nangaso tichite bwanji Mwati padheni ndipiturrr Coz am Mixing drinks and chips chicks kiss, spit, Spilt ma kids on her lips take pix, then take another piss Mwati kwamasteni ndzikaticha? Napalamulaso, akawonela maso , akakalipanso.. Koma ama_nso, ngati ali m'maso apa yalakwanso, Koma aaah Aka ndikachani, aka ka nkazi kandipatsa chiKhumbo aka, akandikachali alah! chemwa_li Ali Tiiwale mavuto ndati nzadziko, ngati malawi_ m'maona kuchedwa nde ma lawi tachita mwamachawi.. Saanakananso , she was a thirsty one nanga Ayi mayi Ananchita mwayi nanji n'nali nawo anayi ; mabotooolo Nantengana m'mafuna nkany*[email protected] naye kenaka ndintaye coz she was digging me Mafosholo Ndayamba kulankhula chizungu, Chizungulile, chizungulileni kuseleku chisungunulileni Chikoke yani, chikokeleni chi mkazichi nchayani chayamba chizunguzime pukupuku matukutuku Kuzunguzuurrr Thukuta, ndachigunditsa kuchipupa chedwela pati kuputurr Zili pakamwazo Sitikamwaso_ ndayaka ndayaka ndayaka!! Kandulo! Ndampatsa mapasa pa mphasa pansi patebulo! sin'gona lero, Opposite ya sober lero Oooh! X2

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com