2035Downloads
Jeff Kaira - Zamanyado
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
VERSE
Anabadwa mwana wokongola
Akamayenda panseu amuna cheucheu
Zochitika zake ndiza changu
Safuna kuvutikila kanthu
Makolo ake akudandaula kunyumba
Sukulu yake anasiyila panjira
Iye kwake nkuyenda yenda mumabala
Akuzisaka zambili zamandede
CHORUS
Amakonda zamanded iyeyo
Amafuna zamanyado iyeyo
Usalimbane naye ameneyo musiye
Amafuna zamanyado iyeyo
VERSE
Ndimatiliyo yenini yinela banja
Amuna amagwada kufunsila banja
Mpaka ena amapeleka malowolo
Koma iyeyo amangoti ine toto
Safuna amuna olila
Safuna amuna ochedwa
Iye afuna amuna opata
Alinazo zambili zamandede
CHORUS
Amakonda zamanded iyeyo
Amafuna zamanyado iyeyo
Usachedwe naye ameneyo iwe musiye
Amafuna zamanyado iyeyo