93079Downloads
Saint - Akazanga
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Verse 1
Munayesetsa kudamager simapeza nazo tulo
Pakamwa panupo ndati zitopotopo kusowa nazo mpumulo
Kwanthawi yaitali mwasokoneza banja langa
Zonyoza zambiri zomangofuna akazi anga
andisiye ine ndekha ndekha ine ndiri padzuwa ine ndikungolira ine mpaka…
Chorus
Aaah… apita akazi anga
Aaah…ayenda adona anga*4
Inu chimwemwe kutsayako
Verse 2
Jus tell me watch want moyo wanga
Poyamba mudandidanitsa ndimakolo anga
Kenako kundidanitsaso ndiabale anga
Ndizanga zonse chifukwa cha inu
Why oh why
Nkhani yakunyumbayi kwanga,imathera pa facebook
Why oh why..
Nkhani yam’banja mwanga,imathera pa whatsapp group
Pamtondo ndipo zimathera nkhani
Zabanja bwanji zikukukhudzani
Ehh,,,Kodi nalakwitsa kukudziwani
mkaziyo mutenge ndinu tchukani
Chorus
Bridge.
Am so lonely,*3
Ndekha ndekha
Am so lonely*4.
Chorus