General Lic - Ondilangiza Analipo (Prod. Thom Gizzo)
Name of album : Ondilangiza Analipo Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro

Haaaa!!! Yah know its ah Warrant Officer Class 1 General Lic, (Classic)

Ondilangiza analipo aaaah/
Sinnamvele malangizowa/
Ndinakomedwa nawo abambowa/
Osadziwa angondi user nkundipotokola/

Chorus

Ondilangiza analipo koma kusamvaaa/
Banja ili n'lazigawenga ndipo n'lambavaaa/
Ndilopanda chisoni anthu ake ndi ankhanzaaa/
Chifukwa chakusamva andisiya mmasanzaaa/

Verse 1

Ankaonetsa umuthu pofuna kundikwatira/
Kulikonse uko ndingapite iye ankandisatira/
Akazi ena omufuna simomwe ankawasasila/
Osadziwa ufumu wakwathu ndiomwe ankausatira/

Chongonditenga ufumu napasidwa/
Chikondi chinachepa chomwe ndinkapatsidwa/
Anayambika mavuto nyumbamo/
Kuiwala Mgwilizano kudana nchilungamo

Anayamba kundisakaa (eheee)/
Zimilandu kundipakaa(oohoo)/
Kukhala chete ndinasakhaa/
Nditangodziwa nduyendedwa ngati (ma card)mpaka/

BTC
Verse 2

Zinayambika ngat macheza/
Kenako kuyamba kutukwanika ndi ana owapeza/
Akakhala ntimagulu basi kuma opsyezaa/
Apa mpomwe bondo ndinanong'oneza/

Anayamba kundipangila ma upo/
Zimilandu mpaka pa bwalo pa amfumupo/

Ndinalira misozi ndikukhetsa/
Amuna anga achakhuli kwa ana anu mundiphetsa/

Ndawalira a x anga a petulo/
Kuyambana ankasiyabe ndalama ya ndiwo pa tebulo/
Ndinkafuna kuwala pano nduchita kusowa ya kendulo/
Katatu sitingadye mulibe ufa okwana mudengulo/

Nnakomedwa ndipakamwa podya za nchele/
Ndinkati uyu ngwa banja osadziwa angofuna andibele/
Nkulingadi utayenda naye kuti udziwe alidele/
Komabe family flag yakwathu ndiyo ndidzafele/

(BTC)

(Bridge)

Anayamba kundisakaa (eheee)/
Zimilandu kundipakaa(oohoo)/
Kukhala chete ndinasakhaa/
Nditangodziwa nduyendedwa ngati (ma card)mpaka/

BTC ×2