Mitso - Imfa Ya Superstar (Prod. Gaffar)
Name of album : Imfa Ya Superstar Genre :Afro-Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO
Aaaaah aaaaah aaaaaaaah!!
De mitso 265, am a 265
Am a superstar
Afriswami yeeeH!!

VERSE 1

mafunyeta anagwa anthu amkati asthma/
Omwewo super star anazima/
Martse kuotcheka ndi moto/ tremor kugundidwa ndi galimoto/
Wary cris achalume/
Akanadwara tikanati akapume/
Koma onsewa ngozi/
Malawi wadzadza ndimagazi/
Chikuchitika ndichani kumpanje/
Kutentha kwathupi taluza nako atoti manje/
Grace chinga anapita mwachidule/
kutisiya zambiri asanaulure/ [kalangaaa!!!]

CHORUS

(Imfa ya super star yomvetsa chisoni ngat usatchuke)×2
Koma ndikaganizira Zima vibe luxury life ndiyera kutchukaaaa!!!

VERSE 2

Imfa ya celeb /
Sungayimvetsetse ngat sentence yopanga verb/
Imakhara yomvetsa chisoni/
Mafunso kuchuluka chachitika mchani/
Umva wagwa ndipo wamwalira /
Fans yonse kusanduka anamalira/
Ine monga oyimba wa ng'ono/
Imfayi imandizizilitsa nkhongono/
Paliponse ululu/
Odandaula amakhala gulu/
Pompopompo ndimabweza gear/
Kupita ku studio ndimadza siya/
[ koma 2 Mina minaaaa!!!!!]