Heptik - Uzaziwa Bwanji ft Mwanache and Murphy
Name of album : Uzaziwa Bwanji Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro


B city L city B city x6

Murphy chibwana! heptik,mwanache!

Oh yeah! oh yeah yeaaaah guttah!


Chorus


Uzadziwa bwanji? We represent Mdubz

We kip it turnup! Turnup!

Uzaziwa bwanji? Malawi on fire!

We kip it blazed up blazed up

Black red green from the motherland & sititaya chikhalidwe each & every city now we murder dem all loard have mercy yaaaaaa oooh loard have mercy yaaa

Verse 1: Heptik



Bcity was a city of dreams kale kale

kuli Young kay incyt ndi azinzake

pano kwangochuluka timafana tongofuna

chizungu sichingalamule dziko la akuda/tiphwanya chitaganya ngati nthawi yasamunda

mukupha btwn guyz guyz simukutha

life ya mu video kumalawi ya shupha

u think ur classic new school rap it aint preaty

copying style from lemmar it aint sick

yaaa ndi bwelele mu chichew ndine oopya ngati Aidz uzindipewa ndife mitunda inu miseseleka

kuimba mukuimba koma guyz sizikumveka

afana a international olo pa channel sapezeka

nyimbozanuzi mwina amamvela ma neighbour omvela nyimbo zako axse ndiochepa

Chorus


Verse 2: Mwanache



Chamba chimene chitu chimadana

nchamba muzapenga ndinu mafana kodi ndiliti munayamba

mukumangonamizana mukamamenya ma free style koma mumazimvera nokha zimene mumakamba

mmafuna ukhala ngati akunja ngati akunja amakuziwani nkomwe aaa inu tasinthani nkoni

ati kubwera ka call tone nso yakunja zanu nanga bwanji aaah inu tasinthani tone

choti mudziwe nchoti you can never be them

try competetion maybe u can try to reach them

komano zomakopela sopano muzingotaya nthawi nyengo yake sipano

kuno ndikumala kuno siku UK

zimene mukukamba zivuta kuti ndikhululuke kodi baxi mmaona ngati nku america

kulibwino muziimbanso ngati evans mereka



Bridge: Murphy


Zaozo zongo copera anawa "mbola"/
Saziwa komwe akulowera anawa so "blind" /anawa ndimabombo crat ona angosocheraaaaa

Chorus