578Downloads
Astabo - Undimamatile
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
(Verse 1)
Usamakhumudwe dzikoli ndi choncho, usamafooke Moyowu ndi choncho, kulakwirana sikulephera, kususulana sikukanika mchikondi, chofunika undigwiritse undikakamile, Chofunika undigwiritse usagive msanga...
(Hook)
Ndimakukonda, Ndimakufiiila, nchifukwa chake ndinena..Undima..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..mati..lirebe iwe..Undima..ma..ma..ma..ma..ma..ma..mati..lirebe iwe eeeh..
Undimamatile ndikumamatile Undimamatile ndikumama.. mamamamatilebe iwee...Tikafika....
(Verse 2)
Pena ndimalakwitsa kukulakwira mnzangawe Pena ndimachita zodzikonda kukuswerako mtima, koma.. kulakwirana sikulephera, kususulana sikukanika mchikondi.. Chofunika undigwiritse undikakamile Chofunika undigwiritse usagive msanga...(back to chorus)
(Bridge)
Undimamatile ndikumamatile Undimamatile ndikumama..mamamama... undimaaaaaaaa, Ndikumaaaaaaa...,.