35239Downloads
Kelvin Sings - Zonse (Prod. Manifest)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Honey iwe zomwe wandimvetsa mtimamu
ah inenenene ah inenenene eeh haa
Honey iwe iiih ntima wako ndiotani iwe iweee
ah inenenene ah inenenene
Ngakhale nkhawa yaing'ono
ako maso alunjike kwa ine
ukusowa chani iwe ndiuze ndikakufikile
pali iwe
BRIDGE
poti mwa anzanga onsewa
mwa amuna onsewa
palibe mamuna amene akumva ngati ine
palibe palibe
poti alibe alibe awa
mphumi ngati ineyo
poti ndinapata
CHORUS
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga
uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2
VERSE 2
ndikutali komwe tikulowela-lowela
But knowing that ive got you by my side
suddenly everything is simplified
mumdima sinzayenda ndekha ine
sungalore iwe
kukawala sindingayende ndekha
sindigalole ine
zonse zomwe ndifuna you got it
plus more!!!
pa iwe ine liuma uuhh darling
I know!!!
BRIDGE
poti mwa anzanga onsewa
mwa amuna onsewa
palibe mamuna amene akumva ngati ine
palibe palibe
poti alibe alibe awa
mphumi ngati ineyo
poti ndinapata
CHORUS
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga
uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2
BRIDGE 2
Umankonda ndani
inee
Ndimamukonda ndani
iwe
Nyimboyi ndi yandani
iwe iwe iwe iwe iwe X3
CHORUS
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
Zonse mwa mmodzi X2
zonse zonse zonse zonse eyaa
ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga
uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2