7061Downloads
Bon Kavala Banda - M'dyelekezi Ngotuzuka
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
chorus
mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka M ngotuzuka. mdyelekezi M ngotuzuka atuzuka kwambiri akawona ine!! amandiona ndili ndi yes ineyo,amanditutumuka mchifukwa chake atuzuzuka akawona ine.
verse 2
adani anga atuzuka akawona ine, alekelenji utuzuka akawona ine?akamaloza mumtengo muli kanthu mchifukwa chake andiloza akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati yehosofati pamaso pa a amon wool! mbuye wanga walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati ayisilayeli pamaso pa iguputo M mmm back to chorus.
verse 3
adani Ako atuzuka akawona,alekelenji utuzuka akawona iwe?akamagenda mumtengo muli kanthu mchifukwa chake atuzuzuka akawona iwe*2 Koma mbuye akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati Daniel mumdzenje lamikango.mbuye wako akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati achina misheck mung'anjo yamotoyo!! chorus fading