65783Downloads
Charisma - Panda [Cover]
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
I got broads in chikwawa
sindisuta ndi mafana
hustle bag yangodzadza
ndizosasuta mafana
embassy kukana
ine makonda kubanda
nkona ndavala bandana
100 bolas in the pocket
embassy kukana
ziutsi Ganja
mpoketimu Danhill
kachaso Ku mpanda
izi ndizausatana
ndishale pambali ndibande
ndaniyo akufuna kubanda
100bolasi in the pocket ×2
(Verse)
I got bolla ya marijuana
sinsuta embassy
Ku sipa fanta
hair cut tangoscana singalowe nkachisi
atha kundibana
am living lavish
eti eti amangothoka rubbish
poti ndikungoshina ngati vanish
won't complain ndikadya mpungadi and look how I finish it
zi embasezi mfana
wailesi sikamba zonama
ufabe utayangana kulila ine ndiliphe kudya nanazi
kufila kuchilla kupugula beer more liquor tiye undipeza chapa corner
kupota kusuta kuseli kwa mpanda kowawa ka ganja ka sinkasiya chifukwa kakukomabe
ndikabanda ndimadya zigege
wapansi kukafika nathenje
kumangofila aile man
inu mumva m'bebe mungotha mandede mubeledwe chelete ndianthu amachete kufa ngati vete mwakachetechete kethekethe mwabetsa zotakata now you will never get it
I got bras for sale gula mabele asamakhuthuke
pota nazi bwaxy tiphika chinsima chokhuthula
dalazi fotseki mchotsedi khutedi ndidyaso buledi
Bridget mhuledi kubedi amakhalila kupanga bend
Hook ×2