3025Downloads
The Very Best - Yoshua Alikuti
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
YOSHUA ALIKUTI
CHICHEWA LYRICS
Verse
Ana a mulungu
Aisiraeli azunzika m'chipululu
Bambo Mose musatayilire
Namalenga ati mulamulire
Lero mwataya chipangano
Kuyamba kupembedza makavalo
Chorus
Alikuti yoswayo
Adzabwera liti
Tifuna chipulumutso
Bridge
Wanyoza mtundu wanga
Iwe walakwa x2
Waphetsa mtundu wanga
Ndati walakwa x2
Back to chorus
Alikuti yosuayo
Adzabwera liti
Tifuna chipulumutso
Sitifuna mose wina
Wankhambakamwa
Wodzatisocheretsa
Second verse
Ulendo wochokera kwa iguputo
Unali wautali
Munatiwolotsa yolodani bwinobwino
Nanga lero bwanji
Kabwino konse upange ulalike utakwera chulu
Namalenga sakondwa nazo
Mphoto yako
Udzalandiliratu
Bridge
Chorus