7940Downloads
KYC Nyimbo - September 2018 (Prod. Malde Beats & W Twice)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Dzulo man, zinachitika dzulo
Ndinali m' maso koma ngati zakutulo
Ndaweruka ku vep ndimwe kamodzi ka botolo
komanso magetsi athima ndiguleko kandulo
Ndipeze tulo, I had a busy day
Ntchito yogwira Monday imapereka busy nde
Barman, botolo lakoli Nde ndizabweza mawa
Nthawi sikulora ndufunika ku ntchito mamawa
Koma, ngakhale kwada ndidzereko kwa Tasha
3 days osamuona koma dzulo anaflasha
Amashala yekha amagela ku MIT
Ndi waku North anangobwelera geli ku BT
Inde ndimankaikira kuti mkaziyu ndi wa zake
Manambala okaikitsa amangoti ndi azinzake
Nambala ya Peter atha kuiseva Mary
Koma ngakhale zili choncho ndayenera ndimuyendere
Koma nditangifika, wachibweza chitseko
Am like babie ndine Kelvin tsegula ndiloweko
Then after 2 minutes, kenako ndakhena
Ali mu nsalu koma pambalipa pali ada ena
She's like, babie I'm sorry don't leave me
Sinapange kalikonse believe me
Am like ase, ndisakhale kapolo
Muli ndi mwayi sinagwiritse ntchito botolo
(Man talking while crying )
Zinandibowa kwambiri, imagine, ada amene anali nawowo, ndi a form 3
And what hurts the most, is that I was the one that paid rent for that house
And before that, namvaso nkhani inaso ah
(Woman on Whatsapp Voice Note)
Thom Thom ukudziwa wapanga zobowa,
nakuuza za Olivia ukapezeka zoti uzikamuuza kyc zoona?
Mesa nakuuza zoti auzana okha ngati akufuna? Zandinyasa zimene wapangazo nde apapa kyc ndizimuyankha kuti chani?
Wachita kunditumizira screenshot ati ineyo nakuuza iweyo that means iweyo unamuuza kyc yo zoti ineyo ndamene ndakuuza eti? Olivia angondikalipira panopa
(Verse 2 - Kyc Nyimbo)
Ndili ndi babie, inavaya ku S.A
Koma nkhani zomwe ndikumva sungadzimvetse
My hommie Thom dzulo wandihalla pa whatsapp
Ati man mbola am like yeah tathoka wassup?
Babie yako Olivia ati ili ndi phaa
Wandiuza ndi cousin wake uja Chippa
Mwina ukukaikira nde ndingovunga screenshot
Am like sh!t koma Mfana wanga anampanga abort
Mwina mkona akuika picture ya baby pa DP
Akumalusa mkamuuza tumizako ka new pic
Kodi bwanji ndimangopleyedwa ngati CD
Mtima wanga ukugunda nditha kugwa ndi BP
Of course, nane ndinakuplayer ndi Tasha
Koma vuto ndiwe unkangondiuza za Russia
Kuvaya ku joni unkati ubwera posachedwa
I was lonely Nde sindikanapangiraso mwina
(Man talking while crying)
I had plans with you, I loved you, but mene zililimu, sindingapangireso mwina I just gotta go
(Outro)
Am heartbroken man
Kyc Nyimbo