5106Downloads
Phyzix - Mumatani (Shano Index & Phyzix) Prod. Zephy

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
(INTRO: Phyzix & Shano Index)
It’s Only Entertainment!
Brain Bang Bang inami head
Mr. Oldies on this (aaaaah aah)
Yeah eh
Very Good Very Good
(VERSE 1: Shano Index)
Dzulo kuvina nde kunandipasa pressure
Kuvina steppy ngati kwathu sindipita
Kuona Queen ata tchena!!!
Kuvina steppy nde kumachita kubeba eh
(aaaaah aah)
Ndufuna ndikuwuzeni ine Zomwe ndaziona dzulo
(aaaaah aah)
Dzulo tinatchila✌️all night ine kuchita kusowa tulo
(Pre Hook: Shano Index)
Ndinali ndi achina Vanessa!
Ine kudabwa zomwe amandionetsa
Amavina zondipatsa pressure
Ine pressure kuzangodabwa pressure!! Eh ×2
(HOOK: Shano Index)
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
(VERSE 2: Phyzix)
Kufika kumalo kodya money/ kwachita kudzadzilatu ngati tsiku la nsika/ Week yonse ndimarunner dancehall ndikuchita kumazimva ngati ine ndi Masicka/ tabwerani mumveko ka verse ka/ pamalo patentha ndavala ka vest ka/ hustle yanga ndinakweza gauge/ ndikudya zindalama maluzi nde ndinawatsika/ zikafika apa kodi mumatani?/ ku malo kuli akazi kuposa ma man/ Chibotolo ichi ndi changa siyani/ ngati mukufuna chanu ndigula si nkhani/ Doloyu wakondwa kodi mwamtani?/ zachibwana sangalore olo one tonne/ brain bang bang ndikudya bang bang/ ndimalingalira bho ndinatsegula company
(HOOK: Shano Index & Phyzix)
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
(VERSE 3: Shano Index)
N'kati Kati movina zitakoma
Ndayiwala ndadutsa m'zokhoma
Dj!!! Fakako Awilo longomba
Wina wandikankhila ku khoma eh
(aaaaah aah)
Ndufuna ndikuwuzeni ine Zomwe ndaziona dzulo
(aaaaah aah)
Dzulo tinatchila✌️all night ine kuchita kusowa tulo
(Pre Hook: Shano Index)
Ndinali ndi achina Priscilla
Wandinong'oneza atiwa silila
Ati sakwanitsa kupilila
Ine kukana mpaka Wachita kulila Eh ×2
(HOOK: Shano Index & Phyzix)
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
AAHAAA A!!
Zikafika Pote!! MUMATANI
EEHEEE E!!
(OUTRO: Phyzix & Shano Index)
Mumatani eh Mumatani
Very Good Very Good
Mumatani abale anga Mumatani?