111181Downloads
Piksy - Kameneka (Prod by Famous)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Produced by FAMOUS
VERSE ONE
Ku Mulanje tikafikeko
Tikakwelere phiri tikatsikenso
Ku Likoma tikadziweko
Kuti mitima yathu ikalinkenso
Mtima wanga sunagundepo
Chonchi ukuthamanga ngati mphepo
Moyo wanga sunadumpheko
Ku mbaliyi moyo wanga sungavutenso
Chiri chonse pamwamba
Mosabisa number yathu ndi yoyamba
Ngini ikufwamba
Si ngini ya wamba
Ndeno sindikudanda
Uwuwu ndi nchere si soda
Izi zokha ziribe ma boarder
Ndakhala ndikusakasaka
Ndeno see zomwe Mbuye wandipatsa...
CHORUS
Kameneka
Kameneka
Kanazula mtima wanga
Ndi kameneka
Kameneka
Kamenekaka
Kanazula mtima wanga
Ndikameneka
VERSE 2
Waisokoneza yanga system
Iyeyu ndi katakwe ineyo ndi victim
Sizingatheke kupanga quit
Poti ndiribe choice akusunga yanga nthiti
Watenthetsa dziko linali cold
Kapena uyuyu ndi ngelo kodi?
Akakhala pafupi I'm never bored
Chikondi ndi ichi pa iye i thank God
Mukafuna ma details
Ndiwatumiza pa email
Koma among all the females
Wabwino ndinasankha ndineyo
Mukafuna ma details
Ndiwatumiza pa email
Koma among all the females
Kanga ndi
CHORUS
Kameneka
Kameneka
Kanazula mtima wanga
Ndi kameneka
Kameneka
Kamenekaka
Kanazula mtima wanga
Ndikameneka
Kukazizira ndi ka mbaula
Umbrella mu Mvula
Kosagulika ndi dollar
Kameneka kandidaula
Kukazizira ndi ka mbaula
Umbrella mu Mvula
Kosagulika ndi dollar
Yeah
Kameneka
Kameneka
Kanazula mtima wanga
Ndikameneka
Kameneka
Kamenekaka
Kanazula mtima wanga
Ndikameneka hey
CHORUS
Kameneka
Kameneka
Kanazula mtima wanga
Ndi kameneka
Kameneka
Kamenekaka
Kanazula mtima wanga
Ndikameneka