Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Sungununu- Angosankhana Okha (Lyrics)
Intro.
Yeah! Lilongwe!
Miyambi Music!
Sungununu Mwana!
Hook.
Angosankhana okha, ife sakutisankha x8
Verse 1 (Janta).
Angosakhana okha, Mwayi apasana okha.
M'kachetete Chete amafuna andisekelezele“tsoka“.
Uphawi sindifuna ndimveni nane!!nane mkhumba geni.
Moyo ngati wachipani wasakho amwene!
Haa! Adha awa sananame
Afuna man! Man! eti ndiwone mazangazime ineyo.
Andifowole muwamve lusonganga aphe.
amaseka aziti nfanayu ndikape.
Koma mwachenjela puzuka mwanjela pozuka.
Tiwonana pogona tiwonana pogona.
Tsakho, dumbo zose ndizawo.
Janta akwanilisa kuyimba ndiphavu!!!!!
Hook.
Angosankhana okha, ife sakutisankha x8
Verse 2(Essim).
(ehe)
Angosankhana okha,mwayi amphanga onkha.
Nthawi zonse andikankha khuma ndili ndekhandekha.
Chabwino mulibe mdziko sankho ndinthu lanyanya.
Angondipenya ngati sandimanya.
Kuyambira ndili nkhanda nkangokula modanda.
Nkaoneka mazoba kwa ana akumipanda.
Ankangotisala ngati mwana wa misala.
Moyo wakadzidzi ongokhalila kubisala.
Aaah! Angosankhana pa chinasi.
zawo zinayera kale anakonzakale kapansi.
Tingofera u celeb basi.
Pochoka ku show tikweranso minbus.
Hook
Angosankhana okha, ife sakutisankha x8